-
Genesis 17:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Mkazi wako Sarai,*+ usamamuitanenso kuti Sarai, chifukwa dzina lake tsopano likhala Sara.* 16 Ndidzamudalitsa ndipo adzakuberekera mwana wamwamuna.+ Iye ndidzamudalitsa moti adzakhala mayi wa mitundu yambiri ya anthu ndi wa mafumu a mitundu yambiri ya anthu.”
-