Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbadwa* zako ngati nyenyezi zakumwamba komanso ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja.+ Ndipo mbadwa yako idzalanda mzinda* wa adani ake.+

  • Deuteronomo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ndipo onani, lero mwachulukadi ngati nyenyezi zakuthambo.+

  • Aroma 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Abulahamu anali ndi chiyembekezo ndiponso chikhulupiriro chakuti adzakhala bambo wa mitundu yambiri, ngakhale kuti zimenezi zinkaoneka kuti nʼzosatheka. Anakhulupirira zimenezi mogwirizana ndi zimene zinanenedwa kuti: “Umu ndi mmene mbadwa* zako zidzakhalire.”+

  • Aheberi 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa chifukwa chimenechi, kuchokera kwa mwamuna mmodzi, amene anali ngati wakufa,+ kunabadwa ana ambirimbiri+ ngati nyenyezi zakumwamba komanso osawerengeka ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena