Ekisodo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mkazi aliyense adzapemphe zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala kwa munthu wokhala naye pafupi ndi kwa mkazi amene akukhala mʼnyumba mwake. Zinthu zimenezi mudzaveke ana anu aamuna ndi ana anu aakazi, ndipo mudzatenge zinthu zambiri za Aiguputo.”+ Salimo 105:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anatulutsa anthu ake atatenga siliva ndi golide.+Ndipo pakati pa mafuko ake panalibe amene anapunthwa panjira.
22 Mkazi aliyense adzapemphe zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala kwa munthu wokhala naye pafupi ndi kwa mkazi amene akukhala mʼnyumba mwake. Zinthu zimenezi mudzaveke ana anu aamuna ndi ana anu aakazi, ndipo mudzatenge zinthu zambiri za Aiguputo.”+
37 Anatulutsa anthu ake atatenga siliva ndi golide.+Ndipo pakati pa mafuko ake panalibe amene anapunthwa panjira.