Yesaya 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimapanga kuwala+ ndiponso ndimabweretsa mdima.+Ndimabweretsa mtendere+ komanso tsoka.+Ine Yehova ndimapanga zonsezi. 2 Akorinto 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Popeza Mulungu ndi amene anati: “Kuwale kuchokera mumdima,”+ ndipo pogwiritsa ntchito nkhope ya Khristu waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudza kudziwa Mulungu.
7 Ndimapanga kuwala+ ndiponso ndimabweretsa mdima.+Ndimabweretsa mtendere+ komanso tsoka.+Ine Yehova ndimapanga zonsezi.
6 Popeza Mulungu ndi amene anati: “Kuwale kuchokera mumdima,”+ ndipo pogwiritsa ntchito nkhope ya Khristu waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudza kudziwa Mulungu.