Genesis 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mulungu anati: “Pakhale kuwala.” Ndipo kuwala+ kunakhalapo. Yeremiya 31:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yehova amene amapereka dzuwa kuti liziwala masana,Amene amaika malamulo oti mwezi ndi nyenyezi ziziwala usiku,Amene amavundula nyanjaKuti mafunde ake achite phokoso,Amene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti:+
35 Yehova amene amapereka dzuwa kuti liziwala masana,Amene amaika malamulo oti mwezi ndi nyenyezi ziziwala usiku,Amene amavundula nyanjaKuti mafunde ake achite phokoso,Amene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti:+