Luka 17:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kumbukirani mkazi wa Loti.+ Aheberi 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo chifukwa cha chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati angabwerere mʼmbuyo, ine sindikondwera naye.”+
38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo chifukwa cha chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati angabwerere mʼmbuyo, ine sindikondwera naye.”+