Aheberi 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:38 Tsiku la Yehova, ptsa. 187-188 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 1512/15/1999, ptsa. 20-21
38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+