Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pambuyo pake, mngelo wa Yehova anakumana ndi Hagara mʼchipululu ali pakasupe wamadzi. Kasupeyo anali panjira yopita ku Shura.+

  • Genesis 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno Hagara anapemphera kwa Yehova* kuti: “Inu ndinu Mulungu amene amaona chilichonse.”+ Ananenanso kuti: “Kodi nanenso pano ndaona amene amatha kundionayo?”

  • Oweruza 6:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Tsopano Gidiyoni anazindikira kuti anali mngelo wa Yehova.+

      Nthawi yomweyo Gidiyoni anati: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Ndaonana ndi mngelo wa Yehova maso ndi maso.”+

  • Yohane 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Palibe munthu amene anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pambali pa Atate*+ ndi amene anafotokoza za Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena