Miyambo 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndinali woyamba kulengedwa ndi Yehova,+Ndinali woyambirira pa zinthu zonse zimene anapanga kalekale kwambiri.+ Miyambo 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa nthawi imeneyo, ine ndinali pambali pake monga mmisiri waluso.+ Iye ankasangalala kwambiri ndi ine+ tsiku ndi tsiku.Ndinkakhala wosangalala pamaso pake nthawi zonse.+
22 Ine ndinali woyamba kulengedwa ndi Yehova,+Ndinali woyambirira pa zinthu zonse zimene anapanga kalekale kwambiri.+
30 Pa nthawi imeneyo, ine ndinali pambali pake monga mmisiri waluso.+ Iye ankasangalala kwambiri ndi ine+ tsiku ndi tsiku.Ndinkakhala wosangalala pamaso pake nthawi zonse.+