Ekisodo 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako Aisiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Panali amuna oyenda pansi pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+ Numeri 1:45, 46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Aisiraeli onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo mu Isiraeli, analembedwa mayina mogwirizana ndi nyumba za makolo awo. 46 Anthu onse amene analembedwa mayina anakwana 603,550.+
37 Kenako Aisiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Panali amuna oyenda pansi pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+
45 Aisiraeli onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo mu Isiraeli, analembedwa mayina mogwirizana ndi nyumba za makolo awo. 46 Anthu onse amene analembedwa mayina anakwana 603,550.+