Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 13:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndidzachulukitsa mbadwa zako* ngati mchenga wapadziko lapansi. Choncho ngati munthu angathe kuwerenga mchengawo, ndiye kuti mbadwa zako* zidzatha kuwerengedwa.+

  • Genesis 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbadwa* zako ngati nyenyezi zakumwamba komanso ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja.+ Ndipo mbadwa yako idzalanda mzinda* wa adani ake.+

  • Genesis 46:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mulungu anamuuza kuti: “Ine ndine Mulungu woona, Mulungu wa bambo ako.+ Usaope kupita ku Iguputo, chifukwa kumeneko ndidzakupangitsa kukhala mtundu waukulu.+

  • Ekisodo 38:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mwamuna aliyense amene anawerengedwa, kuyambira wa zaka 20 kupita mʼtsogolo,+ anapereka hafu ya sekeli potengera muyezo wa sekeli lakumalo oyera.* Anthu onse amene anawerengedwa analipo 603,550.+

  • Numeri 2:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Amenewa ndi Aisiraeli amene mayina awo analembedwa, mogwirizana ndi nyumba ya makolo awo. Asilikali onse amene analembedwa mayina mʼmagulu onse, analipo 603,550.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena