Ekisodo 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Aisiraeli mʼmanja mwa Aiguputo,+ ndipo Aisiraeli anaona Aiguputo atafa mʼmphepete mwa nyanja. Ekisodo 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mafunde amphamvu awakwirira. Amira pansi pa nyanja ngati mwala.+ Salimo 136:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anakutumulira Farao ndi asilikali ake mʼNyanja Yofiira,+Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.
30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Aisiraeli mʼmanja mwa Aiguputo,+ ndipo Aisiraeli anaona Aiguputo atafa mʼmphepete mwa nyanja.
15 Anakutumulira Farao ndi asilikali ake mʼNyanja Yofiira,+Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.