Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndipo iweyo, utenge ndodo yako nʼkutambasula dzanja lako kuloza panyanja kuti nyanjayo igawanike. Ukatero Aisiraeli adutsa pakati panyanja, panthaka youma.

  • Machitidwe 7:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Munthu ameneyo anawatsogolera nʼkutuluka nawo+ ndipo anachita zodabwitsa ndi zizindikiro ku Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndiponso mʼchipululu kwa zaka 40.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena