-
Ekisodo 15:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndi mpweya wotuluka mʼmphuno mwanu, madzi anaunjikana pamodzi.
Madzi oyenda anaima ngati khoma.
Mafunde amphamvu anaundana pakatikati pa nyanja.
-