Ekisodo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi mpweya wotuluka m’mphuno mwanu,+ madzi anaunjikika pamodzi.Madzi oyenda anaima ngati khoma.Madzi amphamvu anaundana pakatikati pa nyanja. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:8 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 26
8 Ndi mpweya wotuluka m’mphuno mwanu,+ madzi anaunjikika pamodzi.Madzi oyenda anaima ngati khoma.Madzi amphamvu anaundana pakatikati pa nyanja.