Ekisodo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako mfumu ya Iguputo inauzidwa kuti Aisiraeli athawa. Nthawi yomweyo mtima wa Farao ndi atumiki ake unasinthanso ataganizira za Aisiraeli,+ moti anati: “Nʼchifukwa chiyani tachita zimenezi? Nʼchifukwa chiyani talola kuti akapolo athu Aisiraeli achoke?” Ekisodo 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aiguputo ankawathamangira,+ ndipo magaleta onse a Farao, asilikali apamahatchi ndi gulu lake lankhondo anawayandikira. Aisiraeliwo anali atamanga msasa mʼmphepete mwa nyanja, pafupi ndi Pihahiroti moyangʼanizana ndi Baala-zefoni.
5 Kenako mfumu ya Iguputo inauzidwa kuti Aisiraeli athawa. Nthawi yomweyo mtima wa Farao ndi atumiki ake unasinthanso ataganizira za Aisiraeli,+ moti anati: “Nʼchifukwa chiyani tachita zimenezi? Nʼchifukwa chiyani talola kuti akapolo athu Aisiraeli achoke?”
9 Aiguputo ankawathamangira,+ ndipo magaleta onse a Farao, asilikali apamahatchi ndi gulu lake lankhondo anawayandikira. Aisiraeliwo anali atamanga msasa mʼmphepete mwa nyanja, pafupi ndi Pihahiroti moyangʼanizana ndi Baala-zefoni.