Ekisodo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma anthuwo anali ndi ludzu kwambiri ndipo anapitiriza kungʼungʼudza motsutsana ndi Mose+ kuti: “Nʼchifukwa chiyani unatitulutsa ku Iguputo kuti udzatiphe ndi ludzu limodzi ndi ana athu ndi ziweto zathu?” Numeri 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi ukuyesa nʼchinthu chachingʼono kuti unatichotsa mʼdziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere mʼchipululu muno?+ Kodi tsopano ukufunanso kuti wotilamulira ukhale iwe wekha?
3 Koma anthuwo anali ndi ludzu kwambiri ndipo anapitiriza kungʼungʼudza motsutsana ndi Mose+ kuti: “Nʼchifukwa chiyani unatitulutsa ku Iguputo kuti udzatiphe ndi ludzu limodzi ndi ana athu ndi ziweto zathu?”
13 Kodi ukuyesa nʼchinthu chachingʼono kuti unatichotsa mʼdziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere mʼchipululu muno?+ Kodi tsopano ukufunanso kuti wotilamulira ukhale iwe wekha?