Levitiko 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwamuna asamagone ndi nyama nʼkukhala wodetsedwa, ndipo mkazi asamadzipereke kwa nyama kuti agone nayo.+ Kuchita zimenezi nʼkosemphana ndi chibadwa. Levitiko 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwamuna akagona ndi nyama, aziphedwa ndithu ndipo muziphanso nyamayo.+ Deuteronomo 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi nyama iliyonse.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
23 Mwamuna asamagone ndi nyama nʼkukhala wodetsedwa, ndipo mkazi asamadzipereke kwa nyama kuti agone nayo.+ Kuchita zimenezi nʼkosemphana ndi chibadwa.
21 ‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi nyama iliyonse.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)