Ekisodo 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Aliyense wogonana ndi nyama, aziphedwa ndithu.+ Deuteronomo 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi nyama iliyonse.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
21 ‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi nyama iliyonse.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)