Levitiko 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza gulu lonse la Aisiraeli kuti, ‘Mukhale oyera, chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+ Numeri 15:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Lamulo limeneli likuthandizani kuti muzikumbukira komanso kusunga malamulo anga onse ndiponso kukhala oyera kwa Mulungu wanu.+ 1 Petulo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mofanana ndi Woyera amene anakuitanani, inunso khalani oyera mʼmakhalidwe anu onse,+
40 Lamulo limeneli likuthandizani kuti muzikumbukira komanso kusunga malamulo anga onse ndiponso kukhala oyera kwa Mulungu wanu.+