16 Ngati simupita nafe, kodi anthu adziwa bwanji kuti ine ndi anthu anuwa mwatikomera mtima? Koma mukapita nafe+ zisonyeza kuti ine ndi anthu anuwa mwatisiyanitsa ndi anthu ena onse amene ali padziko lapansi.”+
21 Iye ndi amene muyenera kumutamanda.+ Iyeyo ndi Mulungu wanu amene wakuchitirani zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha zonsezi, zimene mwaziona ndi maso anu.+