Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma musadye+ nyama limodzi ndi magazi ake,+ chifukwa magaziwo ndi moyo wake.

  • Levitiko 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Musamadye mafuta kapena magazi alionse.+ Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale, kulikonse kumene mungakhale.’”

  • Levitiko 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Munthu aliyense wamʼnyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzadana naye ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake.

  • Deuteronomo 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma musamadye magazi ake.+ Muziwathira pansi ngati madzi.+

  • 1 Samueli 14:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndiyeno anthu ena anauza Sauli kuti: “Anthutu akuchimwira Yehova. Akudya nyama pamodzi ndi magazi ake.”+ Iye anati: “Mwachita zinthu mopanda chikhulupiriro. Gubuduzani chimwala mubwere nacho kuno mwamsanga.”

  • Machitidwe 15:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma tiyeni tiwalembere kuti apewe zinthu zoipitsidwa ndi mafano,+ chiwerewere,*+ zopotola* ndi magazi.+

  • Machitidwe 15:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola*+ ndi chiwerewere.*+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri, zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena