Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Musagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wanu molakwika,+ chifukwa Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina Lake molakwika osamulanga.+

  • Mateyu 5:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti: ‘Musamalumbire koma osachita,+ mʼmalomwake muzikwaniritsa zimene mwalonjeza kwa Yehova.’*+

  • Mateyu 5:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Tangotsimikizani kuti mukati ‘Indeʼ akhaledi inde, ndipo mukati ‘Ayiʼ akhaledi ayi,+ chifukwa mawu owonjezera pamenepa ndi ochokera kwa woipayo.+

  • Yakobo 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Koma koposa zonse abale anga, siyani kulumbira, potchula kumwamba kapena dziko lapansi kapena lumbiro lina lililonse. Koma mukati “Inde,” azikhaladi inde ndipo mukati “Ayi,” azikhaladi ayi+ kuti musakhale oyenera kuweruzidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena