Levitiko 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mwamuna kapena mkazi aliyense amene amalankhula ndi mizimu kapena kulosera zamʼtsogolo* aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa powaponya miyala. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.’” Machitidwe 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno pamene tinkapita kumalo opempherera, tinakumana ndi mtsikana wina wantchito wogwidwa ndi mzimu, chiwanda cholosera zamʼtsogolo.+ Iye ankachititsa kuti mabwana ake azipindula kwambiri chifukwa cha zoloserazo.
27 Mwamuna kapena mkazi aliyense amene amalankhula ndi mizimu kapena kulosera zamʼtsogolo* aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa powaponya miyala. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.’”
16 Ndiyeno pamene tinkapita kumalo opempherera, tinakumana ndi mtsikana wina wantchito wogwidwa ndi mzimu, chiwanda cholosera zamʼtsogolo.+ Iye ankachititsa kuti mabwana ake azipindula kwambiri chifukwa cha zoloserazo.