9 Koma inu ndi “fuko losankhidwa mwapadera, ansembe achifumu, mtundu woyera+ ndiponso anthu oti adzakhale chuma chapadera.+ Mwasankhidwa kuti mulengeze makhalidwe abwino kwambiri”+ a Mulungu amene anakuitanani kuti muchoke mumdima ndipo anakulandirani mʼkuwala kwake kodabwitsa.+