-
Ekisodo 28:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Kachitsuloko kazikhala pamphumi pa Aroni. Munthu akachimwira zinthu zopatulika+ zimene Aisiraeli amaziyeretsa akamazipereka ngati mphatso zopatulika, Aroni aziyankha mlandu wa tchimo limenelo. Kachitsuloko kazikhala pamphumi pake nthawi zonse, kuti azichititsa anthuwo kukhala ovomerezeka pamaso pa Yehova.
-