Numeri 18:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Musachimwe polephera kupereka gawo labwino koposa la zinthuzo, ndipo musaipitse zinthu zopatulika za ana a Isiraeli, kuti mungafe.’”+
32 Musachimwe polephera kupereka gawo labwino koposa la zinthuzo, ndipo musaipitse zinthu zopatulika za ana a Isiraeli, kuti mungafe.’”+