Levitiko 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musamabere anzanu mwachinyengo+ ndipo musamalande zinthu za aliyense.+ Malipiro a munthu waganyu asagone mʼnyumba mwanu mpaka mʼmawa.+ Miyambo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usabere munthu wosauka chifukwa choti ndi wosauka,+Ndipo usapondereze munthu wonyozeka pageti la mzinda,+
13 Musamabere anzanu mwachinyengo+ ndipo musamalande zinthu za aliyense.+ Malipiro a munthu waganyu asagone mʼnyumba mwanu mpaka mʼmawa.+
22 Usabere munthu wosauka chifukwa choti ndi wosauka,+Ndipo usapondereze munthu wonyozeka pageti la mzinda,+