Levitiko 25:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mʼbale wanu amene mukukhala naye pafupi akasauka nʼkudzigulitsa kwa inu,+ musamamugwiritse ntchito ngati kapolo.+ Levitiko 25:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Musamamuchitire nkhanza,+ ndipo muziopa Mulungu wanu.+
39 Mʼbale wanu amene mukukhala naye pafupi akasauka nʼkudzigulitsa kwa inu,+ musamamugwiritse ntchito ngati kapolo.+