Levitiko 25:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Muzimuona ngati waganyu+ komanso ngati mlendo. Azikugwirirani ntchito mpaka Chaka cha Ufulu. Levitiko 25:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Musamamuchitire nkhanza,+ ndipo muziopa Mulungu wanu.+ Akolose 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu anthu amene ndinu ambuye, muzichitira akapolo anu zinthu zachilungamo ndi zoyenera, chifukwa mukudziwa kuti inunso muli ndi Ambuye kumwamba.+
4 Inu anthu amene ndinu ambuye, muzichitira akapolo anu zinthu zachilungamo ndi zoyenera, chifukwa mukudziwa kuti inunso muli ndi Ambuye kumwamba.+