Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yehova Mulungu wanu adzayeretsa* mitima yanu ndi mitima ya ana anu,+ kuti muzikonda Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse komanso moyo wanu wonse ndipo mudzakhala ndi moyo.+

  • Yeremiya 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Chitani mdulidwe pamaso pa Yehova,

      Chitani mdulidwe wa mitima yanu,+

      Inu anthu a ku Yuda komanso anthu amene mukukhala mu Yerusalemu,

      Kuti mkwiyo wanga usayake ngati moto,

      Usayake popanda aliyense wowuzimitsa,

      Chifukwa cha zochita zanu zoipa.”+

  • Machitidwe 7:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Anthu okanika inu ndiponso osachita mdulidwe wamumtima ndi mʼmakutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mukuchita zinthu ngati mmene ankachitira makolo anu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena