Deuteronomo 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova Mulungu wanu adzachita mdulidwe wa mitima yanu+ ndi mitima ya ana anu,+ kuti muzikonda Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse, kuti mukhale ndi moyo.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:6 Nsanja ya Olonda,6/1/2007, tsa. 13
6 Yehova Mulungu wanu adzachita mdulidwe wa mitima yanu+ ndi mitima ya ana anu,+ kuti muzikonda Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse, kuti mukhale ndi moyo.+