Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Munthuyo aziulula+ tchimo limene wachita. Azipereka malipiro onse a mlandu wake, komanso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a malipirowo.+ Azipereka malipirowo kwa munthu amene wamulakwira.

  • Salimo 32:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,

      Sindinabise cholakwa changa.+

      Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+

      Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah)

  • Miyambo 28:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+

      Koma amene amawaulula nʼkuwasiya adzachitiridwa chifundo.+

  • 1 Yohane 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mulungu ndi wokhulupirika ndiponso wolungama, choncho tikavomereza machimo athu, adzatikhululukira komanso kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena