Numeri 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthuyo aziulula+ tchimo lake limene wachita. Azipereka malipiro onse a mlandu wake, komanso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo asanu a malipirowo.+ Azipereka malipirowo kwa munthu amene wam’lakwira.
7 Munthuyo aziulula+ tchimo lake limene wachita. Azipereka malipiro onse a mlandu wake, komanso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo asanu a malipirowo.+ Azipereka malipirowo kwa munthu amene wam’lakwira.