Ekisodo 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu onse amene awerengedwa azipereka zinthu izi: hafu ya sekeli* yofanana ndi sekeli yakumalo oyera.*+ Magera* 20 amakwana sekeli imodzi. Hafu ya sekeli ndi chopereka kwa Yehova.+ Levitiko 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mtengo uliwonse womwe unaikidwa uzikhala wofanana ndi sekeli yakumalo oyera. Sekeli imodzi izikwana magera* 20.
13 Anthu onse amene awerengedwa azipereka zinthu izi: hafu ya sekeli* yofanana ndi sekeli yakumalo oyera.*+ Magera* 20 amakwana sekeli imodzi. Hafu ya sekeli ndi chopereka kwa Yehova.+
25 Mtengo uliwonse womwe unaikidwa uzikhala wofanana ndi sekeli yakumalo oyera. Sekeli imodzi izikwana magera* 20.