2 Mbiri 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatero anauza anthu onse a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho wopatulika+ umene Mose mtumiki wa Mulungu woona analamula Aisiraeli mʼchipululu. Mateyu 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atafika ku Kaperenao, anthu okhometsa msonkho wa madalakima awiri anapita kwa Petulo nʼkumufunsa kuti: “Kodi mphunzitsi wanu amapereka madalakima awiri* a msonkho?”+
9 Atatero anauza anthu onse a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho wopatulika+ umene Mose mtumiki wa Mulungu woona analamula Aisiraeli mʼchipululu.
24 Atafika ku Kaperenao, anthu okhometsa msonkho wa madalakima awiri anapita kwa Petulo nʼkumufunsa kuti: “Kodi mphunzitsi wanu amapereka madalakima awiri* a msonkho?”+