1 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna+ ndipo mutu wa Khristu ndi Mulungu.+ 1 Petulo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mofanana ndi zimenezi, inu akazi muzigonjera amuna anu+ kuti ngati safuna kumvera Mawu a Mulungu, akopeke ndi khalidwe lanu, osati ndi mawu anu+
3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna+ ndipo mutu wa Khristu ndi Mulungu.+
3 Mofanana ndi zimenezi, inu akazi muzigonjera amuna anu+ kuti ngati safuna kumvera Mawu a Mulungu, akopeke ndi khalidwe lanu, osati ndi mawu anu+