-
1 Akorinto 15:27, 28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Mulungu “anaika zinthu zonse pansi pa mapazi ake.”+ Koma pamene akunena kuti ‘waika zinthu zonse pansi pake,’+ nʼzodziwikiratu kuti sakuphatikizapo Mulunguyo, amene anaika zinthu zonsezo pansi pa iye.+ 28 Koma zinthu zonse zikadzakhala pansi pake, Mwanayonso adzasonyeza kuti ali pansi pa ulamuliro wa Mulungu,+ kuti Mulungu akhale zinthu zonse kwa aliyense.+
-