Genesis 29:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho Leya anakhala woyembekezera ndipo anabereka mwana wamwamuna. Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Rubeni,*+ ndipo anati: “Chifukwa Yehova waona kusautsika kwanga,+ ndipo tsopano mwamuna wanga ayamba kundikonda.” Numeri 2:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amene azimanga msasa wawo kumʼmwera ndi gulu la mafuko atatu la Rubeni+ ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri. 11 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 46,500.+
32 Choncho Leya anakhala woyembekezera ndipo anabereka mwana wamwamuna. Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Rubeni,*+ ndipo anati: “Chifukwa Yehova waona kusautsika kwanga,+ ndipo tsopano mwamuna wanga ayamba kundikonda.”
10 Amene azimanga msasa wawo kumʼmwera ndi gulu la mafuko atatu la Rubeni+ ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri. 11 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 46,500.+