Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno chifukwa choti wachimwira malo oyera, azilipira ndipo aziwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a malipirowo.+ Malipirowo aziwapereka kwa wansembe limodzi ndi nkhosa yamphongo ya nsembe yakupalamula, kenako wansembeyo aziphimba machimo+ a munthuyo ndipo adzakhululukidwa.+

  • Levitiko 6:6, 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndipo azibweretsa kwa wansembe nkhosa yamphongo yopanda chilema kuti ikhale nsembe yake yakupalamula, yoperekedwa kwa Yehova, mogwirizana ndi mtengo umene wagamulidwa kuti ikhale nsembe yakupalamula.+ 7 Wansembe aziphimba machimo a munthuyo pamaso pa Yehova, ndipo adzakhululukidwa chilichonse chimene wachita chimene chapangitsa kuti apalamule mlandu.”+

  • Levitiko 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Lamulo la nsembe yakupalamula ndi lofanana ndi la nsembe yamachimo. Nyama ya nsembeyi izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo pophimba machimo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena