Genesis 43:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yosefe atakweza maso ake nʼkuona mngʼono wake Benjamini, mʼbale wake wa mimba imodzi,+ anati: “Kodi uyu ndi mngʼono wanu amene munkanena uja?”+ Ananenanso kuti: “Mulungu akukomere mtima mwana wanga.” Genesis 46:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Benjamini+ anali Bela, Bekeri, Asibeli, Gera,+ Namani, Ehi, Rosi, Mupimu, Hupimu+ ndi Aridi.+ Numeri 2:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako pazibwera fuko la Benjamini. Mtsogoleri wa ana a Benjamini ndi Abidana,+ mwana wa Gidiyoni. 23 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 35,400.+
29 Yosefe atakweza maso ake nʼkuona mngʼono wake Benjamini, mʼbale wake wa mimba imodzi,+ anati: “Kodi uyu ndi mngʼono wanu amene munkanena uja?”+ Ananenanso kuti: “Mulungu akukomere mtima mwana wanga.”
21 Ana a Benjamini+ anali Bela, Bekeri, Asibeli, Gera,+ Namani, Ehi, Rosi, Mupimu, Hupimu+ ndi Aridi.+
22 Kenako pazibwera fuko la Benjamini. Mtsogoleri wa ana a Benjamini ndi Abidana,+ mwana wa Gidiyoni. 23 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 35,400.+