Genesis 29:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Apa tsopano mwamuna wanga andikonda basi, chifukwa ndamuberekera ana aamuna atatu.” Choncho mwanayo anamupatsa dzina lakuti Levi.*+ Genesis 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ana a Levi+ anali Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Numeri 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ine ndasankha Alevi pakati pa Aisiraeli mʼmalo mwa ana onse oyamba kubadwa* a Aisiraeli+ ndipo Aleviwo adzakhala anga.
34 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Apa tsopano mwamuna wanga andikonda basi, chifukwa ndamuberekera ana aamuna atatu.” Choncho mwanayo anamupatsa dzina lakuti Levi.*+
12 “Ine ndasankha Alevi pakati pa Aisiraeli mʼmalo mwa ana onse oyamba kubadwa* a Aisiraeli+ ndipo Aleviwo adzakhala anga.