Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 13:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Iwo anabwerera kwa Mose ndi Aroni ndiponso gulu lonse la Aisiraeli mʼchipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera gulu lonselo za ulendo wawo nʼkuwaonetsa zipatso za kudzikolo.

  • Numeri 20:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Gulu lonse la Aisiraeli linanyamuka ku Kadesi kuja nʼkukafika kuphiri la Hora.+

  • Numeri 33:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Atanyamuka ku Ezioni-geberi anakamanga msasa mʼchipululu cha Zini,+ ku Kadesi.

  • Deuteronomo 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Panadutsa zaka 38 kuti tiyende kuchokera ku Kadesi-barinea nʼkuwoloka chigwa cha Zeredi,* mpaka mʼbadwo wonse wa amuna opita kunkhondo utatha pakati pathu, mogwirizana ndi zimene Yehova analumbira kwa iwo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena