Numeri 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene Aisiraeliwo ankapitiriza ulendo wawo kuchokera kuphiri la Hora+ kudzera njira yopita ku Nyanja Yofiira, pofuna kulambalala dziko la Edomu,+ anthuwo anatopa ndi ulendowo. Numeri 33:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pambuyo pake ananyamuka ku Kadesi, nʼkukamanga msasa kuphiri la Hora,+ kumalire ndi dziko la Edomu.
4 Pamene Aisiraeliwo ankapitiriza ulendo wawo kuchokera kuphiri la Hora+ kudzera njira yopita ku Nyanja Yofiira, pofuna kulambalala dziko la Edomu,+ anthuwo anatopa ndi ulendowo.
37 Pambuyo pake ananyamuka ku Kadesi, nʼkukamanga msasa kuphiri la Hora,+ kumalire ndi dziko la Edomu.