Ekisodo 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno mngelo wa Mulungu woona+ amene ankayenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka nʼkupita kumbuyo kwawo. Ndipo chipilala cha mtambo chija chinachoka kutsogolo nʼkukaima kumbuyo kwawo.+ Ekisodo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndikukutumizirani mngelo patsogolo panu+ kuti azikutetezani mʼnjira komanso kukakulowetsani mʼdziko limene ndakukonzerani.+ Ekisodo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ ndipo ndidzathamangitsa Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
19 Ndiyeno mngelo wa Mulungu woona+ amene ankayenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka nʼkupita kumbuyo kwawo. Ndipo chipilala cha mtambo chija chinachoka kutsogolo nʼkukaima kumbuyo kwawo.+
20 Ndikukutumizirani mngelo patsogolo panu+ kuti azikutetezani mʼnjira komanso kukakulowetsani mʼdziko limene ndakukonzerani.+
2 Ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ ndipo ndidzathamangitsa Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+