Ekisodo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Inu musanafike, ndidzawachititsa kuti azindiopa.+ Ndidzasokoneza anthu onse amene mudzakumane nawo. Ndipo ndidzachititsa kuti adani anu onse agonje nʼkuthawa.*+ Deuteronomo 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adzapereka mafumu awo mʼmanja mwanu,+ ndipo inu mudzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzalimbane ndi inu+ mpaka mutawawononga.+
27 Inu musanafike, ndidzawachititsa kuti azindiopa.+ Ndidzasokoneza anthu onse amene mudzakumane nawo. Ndipo ndidzachititsa kuti adani anu onse agonje nʼkuthawa.*+
24 Adzapereka mafumu awo mʼmanja mwanu,+ ndipo inu mudzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzalimbane ndi inu+ mpaka mutawawononga.+