Ekisodo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi mʼbuku kuti anthu azidzazikumbukira ndipo umuuze Yoswa kuti, ‘Ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi ndipo sadzakumbukiridwa nʼkomwe.’”+ Salimo 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwadzudzula mitundu ya anthu+ ndipo mwawononga anthu oipa,Nʼkufufuta dzina lawo kwamuyaya.
14 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi mʼbuku kuti anthu azidzazikumbukira ndipo umuuze Yoswa kuti, ‘Ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi ndipo sadzakumbukiridwa nʼkomwe.’”+