Numeri 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Balamu ananena ndakatulo yakuti:+ “Balaki mfumu ya Mowabu wandibweretsa kuno kuchokera ku Aramu,+Kuchokera kumapiri akumʼmawa kuti: ‘Bwera, udzanditembererere Yakobo. Bwera, udzaitanire tsoka pa Isiraeli.’+ Numeri 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako analankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Mawu a Balamu mwana wa Beori,Mawu a mwamuna amene maso ake atseguka,
7 Kenako Balamu ananena ndakatulo yakuti:+ “Balaki mfumu ya Mowabu wandibweretsa kuno kuchokera ku Aramu,+Kuchokera kumapiri akumʼmawa kuti: ‘Bwera, udzanditembererere Yakobo. Bwera, udzaitanire tsoka pa Isiraeli.’+
3 Kenako analankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Mawu a Balamu mwana wa Beori,Mawu a mwamuna amene maso ake atseguka,