Numeri 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Balamu ananena ndakatulo yakuti:+ “Balaki mfumu ya Mowabu wandibweretsa kuno kuchokera ku Aramu,+Kuchokera kumapiri akumʼmawa kuti: ‘Bwera, udzanditembererere Yakobo. Bwera, udzaitanire tsoka pa Isiraeli.’+ Numeri 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Balamu anayambanso kulankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Nyamuka, Balaki iwe, tamvera. Ndimvetsere, iwe mwana wa Zipori.
7 Kenako Balamu ananena ndakatulo yakuti:+ “Balaki mfumu ya Mowabu wandibweretsa kuno kuchokera ku Aramu,+Kuchokera kumapiri akumʼmawa kuti: ‘Bwera, udzanditembererere Yakobo. Bwera, udzaitanire tsoka pa Isiraeli.’+
18 Kenako Balamu anayambanso kulankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Nyamuka, Balaki iwe, tamvera. Ndimvetsere, iwe mwana wa Zipori.