Numeri 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Aisiraeli azimanga matenti awo mogwirizana ndi msasa wawo, munthu aliyense mogwirizana ndi gulu lake la mafuko atatu,+ potengera magulu awo.* Numeri 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Aisiraeli azikhoma matenti awo, pamalo amene gulu lawo la mafuko atatu+ lapatsidwa, munthu aliyense azikhala pafupi ndi chizindikiro cha nyumba ya makolo ake. Iwo azikhoma matenti awo mozungulira chihema chokumanako komanso moyangʼana chihemacho.
52 Aisiraeli azimanga matenti awo mogwirizana ndi msasa wawo, munthu aliyense mogwirizana ndi gulu lake la mafuko atatu,+ potengera magulu awo.*
2 “Aisiraeli azikhoma matenti awo, pamalo amene gulu lawo la mafuko atatu+ lapatsidwa, munthu aliyense azikhala pafupi ndi chizindikiro cha nyumba ya makolo ake. Iwo azikhoma matenti awo mozungulira chihema chokumanako komanso moyangʼana chihemacho.